TTB Chichewa Por: Thru the Bible Chichewa Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera pologalamu imodzi patsiku kuyambira lolemba mpaka lachisanu. Ngati mungakwanitse kutsatira ndondomekoyi, pakutha kwa zaka zisanu mudzakhala kuti mwawerenga Baibulo lonse. 261 episodios disponibles Latest episodes of the podcast TTB Chichewa Mostrando página 14 de 14 Chiyambi Cha Bukhu La Levitiko Ndi Za Nsembe Yopsereza 01/11/2023 « Primera ‹ Anterior 1 ... 12 13 14 Share Facebook Twitter LinkedIn